Zimaoneka ngati kufunafuna Mulungu ndi mbali imodzi imene imaonetsera umunthu wathu. Koma kodi munayamba mwadzifunsapo mafunso akuti -“Kodi Mulungu ndi ndani”, kapena “Kodi Mulungu ndi otani kwenikweni?” Nanga zimene timadziwa kwenikweni za iye ndi zotani?