Chipulumutso Chimaperekedwa Mwachisomo Kwa A Yuda Ndi Anthu Amitundu
-
Aroma 9:25-10:10
Close
Kusankhidwa Kwa Israyeli Ndi Mulungu
Ngakhale Mulungu amadana ndi tchimo koma amaleza mtima kupereka mwayi kwa anthu onse kuti adze kwa Iye mwakulapa machimo awo.
Tanthauzo La Dzina La Israyeli Kapena Kuti Chomwe Dzina La Israyeli Liimira
Kristu anadza ku mtundu wa Israyeli ngati mwana amene ndi mu Yuda weniweni. Koma akuimira Israyeli ndi mitundu yonse ya dziko lapansi.
Kutetezedwa Kwa Wokhulupirira
Pamene tikamba nkhani ya chipulumutso ndiye kuti tikukamba za chipulumutso.
Wolengedwa Watsopano
Zinthu zonse zithandizana kuchitira ubwino iwo amene anaitanidwa.
Moyo Wodzazidwa Ndi Mzimu Woyera
Pamene wokhulupirira abvutika pamodzi ndi Kristu, tidzalemekezeka naye pamodzi.
Kuyeretsedwa Kopambana
Ntchito iliyonse ya thupi silandiridwa ndi Mulungu.
Masautso Kapena Kulimbana Pa Moyo Wa Wokhulupirira/Wopulumutsidwa
Chipulumutso ndi kuyeretsedwa zimadza kwa inu kudzera mwa Yesu Kristu.
Zinthu Zomwe Ndi Zotchinga Kapena Kuti Zinthu Zolepheretsa Mmoyo Womasulidwa
Wokhulupirira amatumikira Kristu chifukwa amamukonda Iye.
Ntchito Zoonetsa Chiyero
Mkristu sakhala pa iye yekha pamene ali kapolo wa Mulungu.
Wokhulupirira Akhala Woyeretsedwa Mwa Yesu Kristu
Munthu wotembenuka sangathe kukhala muuchimo popeza anafa ndi kuuka pamodzi ndi Kristu Yesu.