Nkhondo Za Davide Ndi Uchimo Wake Pochita Kalembera Wa Anthu
-
1 Mbiri 20:1-21:30
Close
Nkhondo Zomwe Anamenya Davide
Mkristu ayenera kukhala wamphamvu pofuna kuteteza nyumba yake
Nyimbo Yoyamika Ya Davide Ndi Nkhani Ya Kachisi
Chifundo cha Mulungu chilibe malire
Nkhani Ya Davide Ndi Likasa La Mulungu
Ndikofunika kutumikira Yehova mokondwera, pamene tiika chidwi chathu pakuwerenga ndi kukhala mau a Mulungu.
Davide Ndi Likasa La Mulungu
Kuchita chifuniro cha Mulungu, kumadalira mkhristu
Ulamuliro Wa Davide
Pamene mkristu aganizira zoyenda m,moyo wa Khristu, ayenera kudzipereka kwa Kristuyo.
Mndandanda Wa Maina Ya Makolo Ndi Ulamuliro Wa Sauli
Mulungu kawirikawiri amachotsa moyo wa munthu chifukwa cha uchimo.
Chiyambi Cha Bukhu La Mbiri Ndi Kuona Za Mibadwo Ya Anthu
Mbiri ya mtundu wa Israyeli ikuyamba ndi mfumu Sauli ndi kumaliza ndi Benjamini.
Zitsanzo Za Chikondi Chachikristu
Munthu akakhulupirira Kristu amamumvera pa chinthu china chilichonse.
Chikonzero Ndi Ndondomeko Ya Ulendo Wa Paulo
Akazi akhoza kutumikiranso bwino mumpingo.
Paulo Apitiliza Kufotokonza Za Umboni Wa Utumiki Wake
Chiyanjano cha akristu chimakhala chogawana zinthu za Kristu.