Ntchito Zoonetsa Chiyero
-
Aroma 6:13-23
Close
Wokhulupirira Akhala Woyeretsedwa Mwa Yesu Kristu
Munthu wotembenuka sangathe kukhala muuchimo popeza anafa ndi kuuka pamodzi ndi Kristu Yesu.
Mgwirizano Wa Utsogoleri Wa Adamu Ndi Yesu Kristu
Monga momwe uchimo ukulamulira m'dziko, chisomo nacho chikulamulira kudzera mwakulungamitsidwa ndi Ambuye Yesu Kristu.
Phindu La Chipulumutso
Ife, tanaomboledwa ku mkwiyo wa Mulungu kupyolera mwa Yesu Kristu.
Abrahamu Ndi Davide Anayesedwa Wolungama Mwachikhulupiriro
Mulungu akulonjeza moyo wosatha, onse amene akhulupirira kuti Mulungu anaukitsa Mwana wake m'manda.
Kupezeka Kwa Chilungamo Cha Mulungu
Munthu akadziona kuchimwa, ayenera kudza kwa Mulungu, mwachikhulupiriro mwa Yesu Kristu. Ndipo lamulo lidzathandiza kuyenda m'moyo wachiyero.
Munthu Aliyense Ndi Wochimwa Pamaso Pa Mulungu
Chilungamo cha Mulungu chikhoza kuperekedwa kwa onse wokhulupirira mwa Yesu Kristu.
Kumvomerezeka Kwa Njira Za Mulungu
Chipatala cha uchimo onsewu ndiye kudza kwa Yesu Kristu, mwachikhulupiriro.
Chilango Pa Anthu Achipembedzo Ndi Wodziyeretsa Wokha
Anthu ambiri amadziyeretsa okha, pakhala ndi chiphunzitsitso chabwino, koma osachita chomwe aphunzitsacho.
Kuchoka Kwa Munthu Pamaso Pa Mulungu
Tchimo la chilengedwe limanyazitsa Mulungu, ndipo Mulungu adzapereka chilango ndithu.
Paulo Akhumbitsitsa Kulalikira Mau A Mulungu
Chilengedwe chimaonetsa umulungu ndi cholinga chakuti munthu akasowe chowilungula.