Chikonzero Ndi Ndondomeko Ya Ulendo Wa Paulo
-
Aroma 15:27-16:2
Close
Paulo Apitiliza Kufotokonza Za Umboni Wa Utumiki Wake
Chiyanjano cha akristu chimakhala chogawana zinthu za Kristu.
A Yuda Ndi Amitundu Ali Thupi Limodzi Mwa Kristu
Pamene mtumiki apereka Uthenga Wabwino, Mulungu amapereka Mzimu wake Woyera kuti utsuke moyo wa munthu.
Kuthandiza Mbale Wochepa Chikhulupiriro
Ntchito za mkristu ziyenera kuonetsa chithunzi cha Kristu.
Kuonetsa Chikondi Cha Apa Abale
Akristu ayenera kuchita chotheka kusakhumudwitsana monga mwachikhulupiriro chawo.
Tiona Ntchito Zokaikitsa Za Mkristu
Mkristu wokhwima amakhala ndi abale onse mosabvuta.
Mmene Mkristu Ayenera Kukhalira Ndi Boma
Mkristu abvale Yesu mwa mau a Mulungu.
Kuchitira Umboni Kumpingo Ndi Kudziko Lonse
Uchimo wonse ukuchitika pamene Mulungu akuona ndipo ali ndi mphamvu yotsitsa boma lililonse limene likuchita kusamvera.
Kagwiridwe Ka Ntchito Mumpingo
Wokhulupirira ayenera kukondana ndi chikondi chachibadwidwe.
Paulo Akuumba Mkota Chiphunzitso Chake
Chifuniro cha munthu chimaoneka chabwino pamene moyo wa munthu wakonzekanso
Israyeli Abwezeretsedwa Mchikonzero Cha Mulungu
Israyeli adzatsekedwabe m'maso ndi kuumitsa mitima yawo kufikira nthawi ya mkwatulo.