Kusankhidwa Kwa Israyeli Ndi Mulungu

Ngakhale Mulungu amadana ndi tchimo koma amaleza mtima kupereka mwayi kwa anthu onse kuti adze kwa Iye mwakulapa machimo awo.

Tanthauzo La Dzina La Israyeli Kapena Kuti Chomwe Dzina La Israyeli Liimira

Kristu anadza ku mtundu wa Israyeli ngati mwana amene ndi mu Yuda weniweni. Koma akuimira Israyeli ndi mitundu yonse ya dziko lapansi.

Kutetezedwa Kwa Wokhulupirira

Pamene tikamba nkhani ya chipulumutso ndiye kuti tikukamba za chipulumutso.

Wolengedwa Watsopano

Zinthu zonse zithandizana kuchitira ubwino iwo amene anaitanidwa.

Moyo Wodzazidwa Ndi Mzimu Woyera

Pamene wokhulupirira abvutika pamodzi ndi Kristu, tidzalemekezeka naye pamodzi.

Kuyeretsedwa Kopambana

Ntchito iliyonse ya thupi silandiridwa ndi Mulungu.

Masautso Kapena Kulimbana Pa Moyo Wa Wokhulupirira/Wopulumutsidwa

Chipulumutso ndi kuyeretsedwa zimadza kwa inu kudzera mwa Yesu Kristu.

Zinthu Zomwe Ndi Zotchinga Kapena Kuti Zinthu Zolepheretsa M’moyo Womasulidwa

Wokhulupirira amatumikira Kristu chifukwa amamukonda Iye.

Ntchito Zoonetsa Chiyero

Mkristu sakhala pa iye yekha pamene ali kapolo wa Mulungu.

Wokhulupirira Akhala Woyeretsedwa Mwa Yesu Kristu

Munthu wotembenuka sangathe kukhala muuchimo popeza anafa ndi kuuka pamodzi ndi Kristu Yesu.

M’gwirizano Wa Utsogoleri Wa Adamu Ndi Yesu Kristu

Monga momwe uchimo ukulamulira m'dziko, chisomo nacho chikulamulira kudzera mwakulungamitsidwa ndi Ambuye Yesu Kristu.

Kulembetsa email

Sign up for the TWR360 Newsletter

Access updates, news, Biblical teaching and inspirational messages from powerful Christian voices.

Zikomo polembetsa kuti muzilandira zizidziwiso kuchokera ku TWR360

Zina zofunikira zikusowekera

This site is protected by reCAPTCHA, and the Google Privacy Policy & Terms of Use apply.